1 Mafumu 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nawonso Aisiraeli anasonkhana pamodzi ndipo anatenga zonse zofunikira nʼkupita kukakumana nawo. Aisiraeliwo atamanga msasa kutsogolo kwa Asiriya ankangooneka ngati timagulu tiwiri ta mbuzi, pamene Asiriyawo anadzaza dera lonselo.+
27 Nawonso Aisiraeli anasonkhana pamodzi ndipo anatenga zonse zofunikira nʼkupita kukakumana nawo. Aisiraeliwo atamanga msasa kutsogolo kwa Asiriya ankangooneka ngati timagulu tiwiri ta mbuzi, pamene Asiriyawo anadzaza dera lonselo.+