-
1 Mafumu 20:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Magulu awiriwa anakhala moyangʼanizana mʼmisasa kwa masiku 7. Pa tsiku la 7 nkhondo inayambika ndipo Aisiraeli anapha asilikali oyenda pansi a Asiriya okwana 100,000 tsiku limodzi.
-