-
1 Mafumu 20:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Choncho anavala ziguduli mʼchiuno nʼkumanga zingwe kumutu kwawo. Atatero anapita kwa mfumu ya Isiraeli nʼkunena kuti: “Kapolo wanu Beni-hadadi akupempha kuti, ‘Chonde musandiphe.’” Ahabu anati: “Kodi adakali ndi moyo? Amene ujatu ndi mʼbale wanga.”
-