-
1 Mafumu 20:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Anthuwo anaona kuti chimenechi ndi chizindikiro choti zinthu zikhala bwino, ndipo nthawi yomweyo anaona kuti mfumuyo ikunenadi zochokera mumtima. Choncho anati: “Beni-hadadi ndi mʼbale wanu.” Ahabu atamva zimenezi anati: “Pitani mukamutenge.” Choncho Beni-hadadi anabwera kwa Ahabu ndipo Ahabu anauza anthu kuti akweze Beni-hadadi mʼgaleta.
-