-
1 Mafumu 20:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Choncho mneneriyo anauza mnzakeyo kuti: “Chifukwa sunamvere mawu a Yehova, tikasiyana mkango ukupha.” Atasiyana, mkango unabwera nʼkumupha mnzakeyo.
-