-
1 Mafumu 20:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Ndiyeno anapita kwa munthu wina nʼkumuuza kuti: “Ndimenye!” Munthuyo anamʼmenyadi mpaka kumuvulaza.