-
1 Mafumu 20:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Koma ine mtumiki wanu nditatanganidwa ndi zina, mwadzidzidzi munthu uja anasowa.” Pamenepo mfumu ya Isiraeliyo inamuuza kuti: “Chiweruzo chako nʼchomwecho. Wagamula wekha.”
-