1 Mafumu 20:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi yomweyo, mneneriyo anachotsa kansalu kamene kanali kumaso kwake kaja, ndipo mfumu ya Isiraeliyo inamuzindikira kuti anali mmodzi wa aneneri.+
41 Nthawi yomweyo, mneneriyo anachotsa kansalu kamene kanali kumaso kwake kaja, ndipo mfumu ya Isiraeliyo inamuzindikira kuti anali mmodzi wa aneneri.+