-
1 Mafumu 21:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ahabu anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chakuti ndinauza Naboti wa ku Yezereeli kuti, ‘Ndigulitse munda wako wa mpesa. Kapena ngati ukufuna, ndikupatsa munda wina wa mpesa mʼmalo mwa umenewu.’ Koma wandiyankha kuti, ‘Sindingakupatseni munda wanga wa mpesawu.’”
-