1 Mafumu 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Pita ku Samariya+ ukakumane ndi Ahabu mfumu ya Isiraeli. Iye ali mʼmunda wa mpesa wa Naboti ndipo akufuna kutenga mundawo kuti ukhale wake.
18 “Pita ku Samariya+ ukakumane ndi Ahabu mfumu ya Isiraeli. Iye ali mʼmunda wa mpesa wa Naboti ndipo akufuna kutenga mundawo kuti ukhale wake.