4 Kenako inafunsa Yehosafati kuti: “Kodi tipita limodzi kunkhondo ku Ramoti-giliyadi?” Yehosafati anayankha mfumu ya Isiraeliyo kuti: “Inu ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu anu ndi amodzi ndipo mahatchi anga nʼchimodzimodzi ndi mahatchi anu.”+