1 Mafumu 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho mfumu ya Isiraeli inaitana nduna yapanyumba ya mfumu nʼkuiuza kuti: “Kamutenge Mikaya mwana wa Imula, ndipo ubwere naye mwamsanga.”+
9 Choncho mfumu ya Isiraeli inaitana nduna yapanyumba ya mfumu nʼkuiuza kuti: “Kamutenge Mikaya mwana wa Imula, ndipo ubwere naye mwamsanga.”+