-
1 Mafumu 22:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Aneneri ena onse ankaloseranso zofanana ndi zimenezi. Ankanena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana. Yehova akapereka mzindawo kwa inu mfumu.”
-