1 Mafumu 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Paja ndinakuuzani kuti, ‘Sadzalosera zabwino za ine, koma zoipa.’”+
18 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Paja ndinakuuzani kuti, ‘Sadzalosera zabwino za ine, koma zoipa.’”+