1 Mafumu 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti: “Mʼtsekereni munthu uyu.+ Muzimʼpatsa chakudya chochepa ndi madzi ochepa, mpaka nditabwerako mwamtendere.”’”
27 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti: “Mʼtsekereni munthu uyu.+ Muzimʼpatsa chakudya chochepa ndi madzi ochepa, mpaka nditabwerako mwamtendere.”’”