1 Mafumu 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma Mikaya anati: “Mukakabwerakodi mwamtendere ndiye kuti Yehova sanalankhule nane.”+ Ananenanso kuti: “Anthu inu, mawu angawa muwakumbukire.”
28 Koma Mikaya anati: “Mukakabwerakodi mwamtendere ndiye kuti Yehova sanalankhule nane.”+ Ananenanso kuti: “Anthu inu, mawu angawa muwakumbukire.”