-
1 Mafumu 22:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Nkhani zina zokhudza Yehosafati, mphamvu zake ndiponso mmene anamenyera nkhondo, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda.
-