1 Mafumu 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pa nthawiyo ku Edomu+ kunalibe mfumu. Nduna ndi imene inkalamulira ngati mfumu.+