1 Mafumu 22:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ahaziya+ mwana wa Ahabu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya mʼchaka cha 17 cha Yehosafati mfumu ya Yuda ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri.
51 Ahaziya+ mwana wa Ahabu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya mʼchaka cha 17 cha Yehosafati mfumu ya Yuda ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri.