-
2 Mafumu 17:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Zitatero, mfumu ya Asuri inalamula kuti: “Mutumize mmodzi mwa ansembe amene munawagwira kuti abwerere azikakhala kumeneko ndipo akaphunzitse anthuwo chipembedzo cha Mulungu wa mʼderalo.”
-