2 Mafumu 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mmodzi mwa ansembe amene anatengedwa kuchokera ku Samariya, anabwerera nʼkumakakhala ku Beteli.+ Iye ankawaphunzitsa kuopa* Yehova.+
28 Choncho mmodzi mwa ansembe amene anatengedwa kuchokera ku Samariya, anabwerera nʼkumakakhala ku Beteli.+ Iye ankawaphunzitsa kuopa* Yehova.+