2 Mafumu 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komabe mtundu uliwonse unapanga mulungu wake nʼkukamuika* mʼkachisi pamalo okwezeka amene Asamariya anamanga. Mtundu uliwonse unachita zimenezi mʼmizinda imene unkakhala.
29 Komabe mtundu uliwonse unapanga mulungu wake nʼkukamuika* mʼkachisi pamalo okwezeka amene Asamariya anamanga. Mtundu uliwonse unachita zimenezi mʼmizinda imene unkakhala.