2 Mafumu 17:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngakhale kuti anthuwo ankaopa Yehova, anasankha anthu wamba kuti akhale ansembe amʼmalo okwezeka, kuti aziwatumikira mu akachisi pamalo okwezeka.+
32 Ngakhale kuti anthuwo ankaopa Yehova, anasankha anthu wamba kuti akhale ansembe amʼmalo okwezeka, kuti aziwatumikira mu akachisi pamalo okwezeka.+