2 Mafumu 17:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma Yehova amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ndi mphamvu zazikulu ndiponso mkono wamphamvu,*+ ndi amene muyenera kumuopa,+ kumugwadira komanso kupereka nsembe kwa iye.
36 Koma Yehova amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ndi mphamvu zazikulu ndiponso mkono wamphamvu,*+ ndi amene muyenera kumuopa,+ kumugwadira komanso kupereka nsembe kwa iye.