2 Mafumu 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Nthawi zonse muzitsatira mosamala malamulo, ziweruzo ndiponso Chilamulo chimene anakulemberani+ ndipo musamaope milungu ina.
37 Nthawi zonse muzitsatira mosamala malamulo, ziweruzo ndiponso Chilamulo chimene anakulemberani+ ndipo musamaope milungu ina.