2 Mafumu 17:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mitundu imeneyi inkaopa Yehova,+ koma inkatumikiranso zifaniziro zawo zogoba. Mpaka lero, ana awo ndi zidzukulu zawo akuchitabe zimene makolo awo ankachita. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:41 Nsanja ya Olonda,12/1/1990, tsa. 3
41 Mitundu imeneyi inkaopa Yehova,+ koma inkatumikiranso zifaniziro zawo zogoba. Mpaka lero, ana awo ndi zidzukulu zawo akuchitabe zimene makolo awo ankachita.