2 Mafumu 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ankachita zoyenera pamaso pa Yehova,+ ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+