2 Mafumu 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Hezekiya sanamusiye Yehova+ ndipo anapitiriza kumutsatira. Sanasiye kusunga malamulo amene Yehova analamula Mose.
6 Hezekiya sanamusiye Yehova+ ndipo anapitiriza kumutsatira. Sanasiye kusunga malamulo amene Yehova analamula Mose.