2 Mafumu 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiye ubetcherane ndi mbuye wanga mfumu ya Asuri ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti tione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.+
23 Ndiye ubetcherane ndi mbuye wanga mfumu ya Asuri ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti tione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.+