-
2 Mafumu 18:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kodi ukuganiza kuti ndabwera kudzawononga malowa popanda chilolezo cha Yehova? Yehova weniweniyo wandiuza kuti, ‘Pita ukamenyane ndi dzikolo ndipo ukaliwononge.’”
-