2 Mafumu 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova, pokuuzani kuti: “Ndithu Yehova atipulumutsa ndipo mzindawu superekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.”+
30 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova, pokuuzani kuti: “Ndithu Yehova atipulumutsa ndipo mzindawu superekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.”+