2 Mafumu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiika maganizo mwa iye ndipo adzamva nkhani inayake nʼkubwerera kudziko lake. Ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga mʼdziko lakelo.”’”+
7 Ndiika maganizo mwa iye ndipo adzamva nkhani inayake nʼkubwerera kudziko lake. Ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga mʼdziko lakelo.”’”+