2 Mafumu 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndamva pemphero lako+ lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+
20 Ndiyeno Yesaya mwana wa Amozi anatumiza uthenga kwa Hezekiya, wakuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndamva pemphero lako+ lokhudza Senakeribu mfumu ya Asuri.+