-
2 Mafumu 19:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena:
“Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza ndipo wakunyodola.
Mwana wamkazi wa Yerusalemu wakupukusira mutu.
-