2 Mafumu 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi sunamve? Ndinakonza kalekale zimene ndidzachite.+ Ndinakonza zimenezi mʼmasiku amakedzana.+ Tsopano ndizichita.+ Iweyo udzasandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kukhala milu ya mabwinja.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2024, tsa. 30 Nsanja ya Olonda,8/15/1999, tsa. 14
25 Kodi sunamve? Ndinakonza kalekale zimene ndidzachite.+ Ndinakonza zimenezi mʼmasiku amakedzana.+ Tsopano ndizichita.+ Iweyo udzasandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kukhala milu ya mabwinja.+