2 Mafumu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu okhala mʼmizindayo adzafooka.Adzachita mantha ndiponso adzachititsidwa manyazi. Adzakhala ngati zomera zakutchire komanso ngati udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga umene wawauka ndi mphepo yotentha yakumʼmawa.
26 Anthu okhala mʼmizindayo adzafooka.Adzachita mantha ndiponso adzachititsidwa manyazi. Adzakhala ngati zomera zakutchire komanso ngati udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga umene wawauka ndi mphepo yotentha yakumʼmawa.