29 Ichi chidzakhala chizindikiro chanu: Chaka chino mudya mbewu zimene zamera zokha. Mʼchaka chachiwiri mudzadya mbewu zophuka kuchokera ku mbewu zimenezi.+ Koma mʼchaka chachitatu, mudzadzala mbewu nʼkukolola ndipo mudzalima minda ya mpesa nʼkudya zipatso zake.+