2 Mafumu 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yesaya anati: “Bweretsani keke ya nkhuyu zouma.” Choncho iwo anabweretsadi nʼkuiika pachotupa* chimene Hezekiya anali nacho ndipo anayamba kuchira.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:7 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 25
7 Kenako Yesaya anati: “Bweretsani keke ya nkhuyu zouma.” Choncho iwo anabweretsadi nʼkuiika pachotupa* chimene Hezekiya anali nacho ndipo anayamba kuchira.+