-
2 Mafumu 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Atatero Yesaya anafunsa kuti: “Aona chiyani mʼnyumba mwanu?” Hezekiya anayankha kuti: “Aona chilichonse chimene chili mʼnyumba mwanga. Palibe chimene sindinawaonetse pa chuma changa.”
-