2 Mafumu 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu otsala pa cholowa changa+ ndidzawasiya ndipo ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo. Iwo pamodzi ndi katundu wawo adzatengedwa ndi adani awo onse.+
14 Anthu otsala pa cholowa changa+ ndidzawasiya ndipo ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo. Iwo pamodzi ndi katundu wawo adzatengedwa ndi adani awo onse.+