2 Mafumu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼchaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, mfumuyo inatuma Safani mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu yemwe anali mlembi, kuti apite kunyumba ya Yehova.+ Inamuuza kuti:
3 Mʼchaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, mfumuyo inatuma Safani mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu yemwe anali mlembi, kuti apite kunyumba ya Yehova.+ Inamuuza kuti: