2 Mafumu 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Azipereke kwa omwe asankhidwa kuti aziyangʼanira ntchito panyumba ya Yehova, kuti akazipereke kwa amene akugwira ntchitoyo mʼnyumba ya Yehova, kuti akonze* nyumbayo.+
5 Azipereke kwa omwe asankhidwa kuti aziyangʼanira ntchito panyumba ya Yehova, kuti akazipereke kwa amene akugwira ntchitoyo mʼnyumba ya Yehova, kuti akonze* nyumbayo.+