2 Mafumu 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akazipereke kwa amisiri, kwa omanga nyumba ndiponso kwa amisiri omanga ndi miyala. Agulirenso matabwa ndi miyala yosema kuti akonzere nyumbayo.+
6 Akazipereke kwa amisiri, kwa omanga nyumba ndiponso kwa amisiri omanga ndi miyala. Agulirenso matabwa ndi miyala yosema kuti akonzere nyumbayo.+