2 Mafumu 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Safani mlembi anapita kwa mfumu kukanena kuti: “Atumiki anu akhuthula ndalama zimene anazipeza mʼnyumbayo ndipo azipereka kwa omwe anasankhidwa kuti aziyangʼanira ntchito panyumba ya Yehova.”+
9 Ndiyeno Safani mlembi anapita kwa mfumu kukanena kuti: “Atumiki anu akhuthula ndalama zimene anazipeza mʼnyumbayo ndipo azipereka kwa omwe anasankhidwa kuti aziyangʼanira ntchito panyumba ya Yehova.”+