2 Mafumu 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Safani mlembi anauzanso mfumuyo kuti: “Wansembe Hilikiya wandipatsa buku+ linalake.” Ndiyeno Safani anayamba kuwerengera mfumu bukulo.
10 Safani mlembi anauzanso mfumuyo kuti: “Wansembe Hilikiya wandipatsa buku+ linalake.” Ndiyeno Safani anayamba kuwerengera mfumu bukulo.