2 Mafumu 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ansembe a malo okwezekawo sankatumikira kuguwa lansembe la Yehova ku Yerusalemu.+ Koma ankadya mikate yopanda zofufumitsa limodzi ndi abale awo.
9 Ansembe a malo okwezekawo sankatumikira kuguwa lansembe la Yehova ku Yerusalemu.+ Koma ankadya mikate yopanda zofufumitsa limodzi ndi abale awo.