2 Mafumu 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso inaletsa mahatchi amene mafumu a Yuda anawapereka kwa dzuwa kuti asamalowenso mʼnyumba ya Yehova kudzera mʼchipinda chodyera cha Natani-meleki, nduna yapanyumba ya mfumu, chimene chinali pakhonde. Inatenthanso pamoto magaleta a dzuwa.+
11 Komanso inaletsa mahatchi amene mafumu a Yuda anawapereka kwa dzuwa kuti asamalowenso mʼnyumba ya Yehova kudzera mʼchipinda chodyera cha Natani-meleki, nduna yapanyumba ya mfumu, chimene chinali pakhonde. Inatenthanso pamoto magaleta a dzuwa.+