2 Mafumu 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pasika ngati ameneyu anali asanachitikepo kuyambira mʼmasiku amene oweruza ankaweruza Isiraeli komanso mʼmasiku onse a mafumu a Isiraeli ndi mafumu a Yuda.+
22 Pasika ngati ameneyu anali asanachitikepo kuyambira mʼmasiku amene oweruza ankaweruza Isiraeli komanso mʼmasiku onse a mafumu a Isiraeli ndi mafumu a Yuda.+