2 Mafumu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mʼmasiku a Yehoyakimu, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzamenyana naye. Ndipo Yehoyakimu anakhala mtumiki wake kwa zaka zitatu, koma kenako anamugalukira. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:1 Ulosi wa Danieli, ptsa. 31-32
24 Mʼmasiku a Yehoyakimu, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzamenyana naye. Ndipo Yehoyakimu anakhala mtumiki wake kwa zaka zitatu, koma kenako anamugalukira.