2 Mafumu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho iye anatenga Yehoyakini+ nʼkupita naye ku Babulo.+ Ku Yerusalemu anatenganso mayi a mfumuyo, akazi ake, nduna za panyumba yake komanso akuluakulu a mʼdzikolo, nʼkupita nawo ku Babulo. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:15 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 29
15 Choncho iye anatenga Yehoyakini+ nʼkupita naye ku Babulo.+ Ku Yerusalemu anatenganso mayi a mfumuyo, akazi ake, nduna za panyumba yake komanso akuluakulu a mʼdzikolo, nʼkupita nawo ku Babulo.